Ekisodo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Palibe munthu amene ayenera kudzakhudza wolakwayo, chifukwa adzaponyedwa miyala kapena kulasidwa ndithu. Kaya ndi nyama kapena munthu, sadzayenera kukhala ndi moyo.’+ Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira,+ anthu onse ayandikire kuphiri.” Aheberi 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti lamulo lija linawakulira, lakuti: “Nyama iliyonse imene ingakhudze phirilo, iponyedwe miyala.”+
13 Palibe munthu amene ayenera kudzakhudza wolakwayo, chifukwa adzaponyedwa miyala kapena kulasidwa ndithu. Kaya ndi nyama kapena munthu, sadzayenera kukhala ndi moyo.’+ Lipenga la nyanga ya nkhosa likalira,+ anthu onse ayandikire kuphiri.”
20 Pakuti lamulo lija linawakulira, lakuti: “Nyama iliyonse imene ingakhudze phirilo, iponyedwe miyala.”+