Salimo 31:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuikiza mzimu* wanga m’manja mwanu.+Mwandiwombola,+ inu Yehova, Mulungu wachoonadi.+ Aroma 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tikudziwa kuti Mulungu amaweruza anthu amene amachita zimenezi kuti ndi oyenera kulandira chilango ndipo chiweruzo chake ndi chogwirizana ndi choonadi.+
2 Tikudziwa kuti Mulungu amaweruza anthu amene amachita zimenezi kuti ndi oyenera kulandira chilango ndipo chiweruzo chake ndi chogwirizana ndi choonadi.+