Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsopano, imani pomwepa kuti muonenso chinthu chachikuluchi chimene Yehova achite pamaso panu.

  • 2 Samueli 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndi mtundu uti padziko lapansi umene ungafanane ndi mtundu wa anthu anu Aisiraeli,+ amene inu Mulungu munawawombola monga anthu anu+ ndi kudzipangira dzina,+ amene munawachitira zinthu zazikulu ndi zochititsa mantha?+ Munapitikitsa mitundu ina ndi milungu yawo, chifukwa cha anthu anu amene munawawombola+ nokha kuchokera ku Iguputo.

  • 1 Mbiri 17:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndi mtundu winanso uti padziko lapansi umene ungafanane ndi mtundu wa anthu anu Aisiraeli,+ amene inu Mulungu woona munawawombola monga anthu anu,+ ndi kudzipangira dzina mwa kuchita zinthu zazikulu+ ndi zochititsa mantha, popitikitsa mitundu+ pamaso pa anthu anu amene munawawombola ku Iguputo?

  • Salimo 147:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Sanachite zimenezi ndi mtundu wina uliwonse,+

      Ndipo mitundu inayo sikudziwa zigamulo zake.+

      Tamandani Ya, anthu inu!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena