Ekisodo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+ Numeri 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pasatsaleko iliyonse yoti ifike m’mawa,+ ndipo asaphwanye fupa lake lililonse.+ Aikonze motsatira malamulo onse a pasika.+
10 Koma musadzasiye nyama iliyonse kuti ifike m’mawa. Iliyonse yotsala kufika m’mawa mudzaipsereze pamoto.+
12 Pasatsaleko iliyonse yoti ifike m’mawa,+ ndipo asaphwanye fupa lake lililonse.+ Aikonze motsatira malamulo onse a pasika.+