Deuteronomo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ukatenge zina mwa zipatso zoyambirira+ pa zipatso zonse za m’munda mwako zimene udzakolola m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa. Ukaziike m’dengu ndi kupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuika dzina lake.+ Nehemiya 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tinachita maerewo kuti tipezenso wobweretsa kunyumba ya Yehova zipatso zoyamba kucha m’dziko lathu+ chaka ndi chaka, ndi zipatso zoyamba kucha mwa zipatso zonse za mtengo uliwonse.+ Miyambo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+ Ezekieli 44:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso zonse zabwino kwambiri zoyambirira za mtundu uliwonse ndi zopereka zanu zonse za mtundu uliwonse zabwino kwambiri zidzakhala za ansembe.+ Ufa wanu wamisere wochokera ku mbewu zanu zoyambirira muziupereka kwa wansembe+ kuti madalitso abwere panyumba yanu.+
2 ukatenge zina mwa zipatso zoyambirira+ pa zipatso zonse za m’munda mwako zimene udzakolola m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa. Ukaziike m’dengu ndi kupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuika dzina lake.+
35 Tinachita maerewo kuti tipezenso wobweretsa kunyumba ya Yehova zipatso zoyamba kucha m’dziko lathu+ chaka ndi chaka, ndi zipatso zoyamba kucha mwa zipatso zonse za mtengo uliwonse.+
9 Uzilemekeza Yehova ndi zinthu zako zamtengo wapatali+ ndiponso ndi zipatso zako zonse zoyambirira.+
30 Zipatso zonse zabwino kwambiri zoyambirira za mtundu uliwonse ndi zopereka zanu zonse za mtundu uliwonse zabwino kwambiri zidzakhala za ansembe.+ Ufa wanu wamisere wochokera ku mbewu zanu zoyambirira muziupereka kwa wansembe+ kuti madalitso abwere panyumba yanu.+