Ekisodo 34:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako ana onse a Isiraeli anamuyandikira, ndipo iye anayamba kuwauza malamulo onse amene Yehova anam’patsa paphiri la Sinai.+ Aroma 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pajatu akumva chabe chilamulo si amene amakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma otsatira+ chilamulo ndiwo adzayesedwa olungama.+ Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, n’kumadzinyenga ndi maganizo onama.+
32 Kenako ana onse a Isiraeli anamuyandikira, ndipo iye anayamba kuwauza malamulo onse amene Yehova anam’patsa paphiri la Sinai.+
13 Pajatu akumva chabe chilamulo si amene amakhala olungama pamaso pa Mulungu, koma otsatira+ chilamulo ndiwo adzayesedwa olungama.+