-
Ekisodo 26:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Uike zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe pansalu yakumapeto kwenikweni kwa nsalu za chihema zolumikizanazo. Uikenso zingwe zopota 50 zokolekamo ngowe kumapeto kwa nsalu zina zolumikizana, pomwe magulu awiri a nsalu zolumikizanalumikizanazo adzakumane.
-