Ekisodo 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Upange zitsulo 40 zasiliva zamphako+ zokhazikapo mafelemu 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.
19 “Upange zitsulo 40 zasiliva zamphako+ zokhazikapo mafelemu 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.