-
Ekisodo 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Chotero Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kuchita ndendende mmene Yehova anawalamulira. Pamenepo Aroni anaponya ndodo yake patsogolo pa Farao ndi atumiki ake, ndipo ndodoyo inasanduka njoka yaikulu.
-