Ekisodo 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 tebulo+ ndi zipangizo zake zonse ndi mitengo yake yonyamulira, mkate wachionetsero,+ Ekisodo 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’chihemacho udzaikemonso tebulo+ ndi kuikapo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemonso choikapo nyale+ ndi kuyatsa nyale zake.+
4 M’chihemacho udzaikemonso tebulo+ ndi kuikapo zinthu zake mwadongosolo. Kenako udzaikemonso choikapo nyale+ ndi kuyatsa nyale zake.+