Ekisodo 26:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Kenako uike tebulo kunja kwa nsalu yotchinga ndipo uikekonso choikapo nyale.+ Chimenechi chikhale moyang’anizana ndi tebulo kumbali ina ya chihema chopatulika, chakum’mwera. Tebulo uliike chakumpoto.
35 “Kenako uike tebulo kunja kwa nsalu yotchinga ndipo uikekonso choikapo nyale.+ Chimenechi chikhale moyang’anizana ndi tebulo kumbali ina ya chihema chopatulika, chakum’mwera. Tebulo uliike chakumpoto.