Ekisodo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Upangenso sefa wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana,+ ndipo pasefayo upange mphete zinayi zamkuwa m’makona ake anayi.
4 Upangenso sefa wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana,+ ndipo pasefayo upange mphete zinayi zamkuwa m’makona ake anayi.