Ekisodo 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Upangenso nsanamira zake 20 ndi zitsulo zamkuwa 20 zamphako zokhazikapo nsanamirazo. Tizitsulo tokolowekapo nsalu ndi mfundo zake zikhale zasiliva.+ Numeri 3:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo anali kusamaliranso nsanamira+ za mpanda wozungulira bwalo ndiponso zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ komanso zikhomo ndi zingwe zake zolimbitsira nsanamirazo.
10 Upangenso nsanamira zake 20 ndi zitsulo zamkuwa 20 zamphako zokhazikapo nsanamirazo. Tizitsulo tokolowekapo nsalu ndi mfundo zake zikhale zasiliva.+
37 Iwo anali kusamaliranso nsanamira+ za mpanda wozungulira bwalo ndiponso zitsulo zokhazikapo nsanamirazo,+ komanso zikhomo ndi zingwe zake zolimbitsira nsanamirazo.