Ekisodo 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nsanamira zake 20 ndi zitsulo 20 zamphako zokhazikapo nsanamirazo zinali zamkuwa. Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.+
10 Nsanamira zake 20 ndi zitsulo 20 zamphako zokhazikapo nsanamirazo zinali zamkuwa. Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.+