Numeri 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amowabu anachita mantha kwambiri ndi anthuwo chifukwa cha kuchuluka kwawo. Iwo anagwidwa mantha aakulu poopa ana a Isiraeliwo.+ Salimo 105:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+
3 Amowabu anachita mantha kwambiri ndi anthuwo chifukwa cha kuchuluka kwawo. Iwo anagwidwa mantha aakulu poopa ana a Isiraeliwo.+
24 Mulungu anachititsa anthu ake kuberekana,+Ndipo pang’onopang’ono anawasandutsa anthu amphamvu kuposa adani awo.+