Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 26:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Upange zitsulo 40 zasiliva zamphako+ zokhazikapo mafelemu 20 aja. Zitsulo ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zitsulo zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.

  • Ekisodo 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakhale mafelemu 8 ndi zitsulo zasiliva zokhazikapo mafelemu. Zitsulo 16 zokhazikapo mafelemu, ziwiri zikhale pansi pa felemu limodzi la mano awiri, zinanso ziwiri pansi pa felemu lina la mano awiri.

  • Ekisodo 26:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Nsalu imeneyi uipachike pamizati inayi ya mtengo wa mthethe yokutidwa ndi golide. Tizitsulo tokolowekapo nsaluyi tikhale tagolide. Mizati imeneyi ikhale pazitsulo zinayi zasiliva zamphako.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena