Ekisodo 38:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Guwalo analipangiranso sefa wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana. Analowetsa sefayo cha pakati pa guwa lansembe, m’munsi mwa mkombero.+
4 Guwalo analipangiranso sefa wa zitsulo zamkuwa zolukanalukana. Analowetsa sefayo cha pakati pa guwa lansembe, m’munsi mwa mkombero.+