Numeri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene msasa ukusamuka, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihema. Mmenemo, azichotsa nsalu yotchinga+ n’kuphimba nayo likasa+ la umboni. Aheberi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+ Aheberi 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+
5 Pamene msasa ukusamuka, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihema. Mmenemo, azichotsa nsalu yotchinga+ n’kuphimba nayo likasa+ la umboni.
3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+
20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+