Ekisodo 36:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako anapanga nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi anapetapo akerubi.+ Aheberi 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+
35 Kenako anapanga nsalu yotchinga+ ya ulusi wabuluu, ya ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri. Pansaluyi anapetapo akerubi.+
20 Iye ndi amene anatikhazikitsira njira imeneyi monga njira yatsopano ndi yamoyo, yodutsa nsalu yotchinga,+ imene ndi thupi lake.+