Ekisodo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe,+ mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+ Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+
10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe,+ mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+
2 Pakuti panamangidwa chipinda choyamba cha chihema.+ M’chipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo,+ ndi mitanda ya mkate woonetsedwa,+ ndipo chinali kutchedwa “Malo Oyera.”+