Ekisodo 29:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 “Chotero ndidzaonekera pamenepo kwa ana a Isiraeli, ndipo malo amenewa adzayeretsedwa ndi ulemerero wanga.+ 2 Mbiri 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona.
43 “Chotero ndidzaonekera pamenepo kwa ana a Isiraeli, ndipo malo amenewa adzayeretsedwa ndi ulemerero wanga.+
14 Chifukwa cha mtambowo,+ ansembewo analephera kupitiriza kutumikira, popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Mulungu woona.