Numeri 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano m’chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni. Nehemiya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 inuyo simunawasiye m’chipululu chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Mtambo woima njo ngati chipilala sunawachokere usana ndipo unali kuwatsogolera,+ ngakhalenso moto woima njo ngati chipilala sunawachokere usiku ndipo unali kuwaunikira njira imene anayenera kuyendamo.+
11 Tsopano m’chaka chachiwiri, mwezi wachiwiri, pa tsiku la 20,+ mtambo uja unanyamuka pamwamba pa chihema+ cha Umboni.
19 inuyo simunawasiye m’chipululu chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Mtambo woima njo ngati chipilala sunawachokere usana ndipo unali kuwatsogolera,+ ngakhalenso moto woima njo ngati chipilala sunawachokere usiku ndipo unali kuwaunikira njira imene anayenera kuyendamo.+