Ekisodo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso, muwauze kuti chiwerengero cha njerwa zofunika chikhale chakale chomwe chija. Musawachepetsere chiwerengerocho, chifukwa ayamba ulesi.+ N’chifukwa chake akulira kuti, ‘Tikufuna tipite kukapereka nsembe kwa Mulungu wathu!’+
8 Komanso, muwauze kuti chiwerengero cha njerwa zofunika chikhale chakale chomwe chija. Musawachepetsere chiwerengerocho, chifukwa ayamba ulesi.+ N’chifukwa chake akulira kuti, ‘Tikufuna tipite kukapereka nsembe kwa Mulungu wathu!’+