Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Genesis 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
4 Adzakupatsa iwe ndi mbewu zako+ madalitso amene analonjeza Abulahamu,+ kuti udzakhale mwini dziko limene ukukhalamo ngati mlendo,+ limene Mulungu anapatsa Abulahamu.”+