Genesis 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo Nowa anachita zonse motsatira zimene Mulungu anamulamula. Anachitadi momwemo.+ Ekisodo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo.
28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo.