Ekisodo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao pakuti ndalola iye pamodzi ndi atumiki ake kuumitsa mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+ 1 Samueli 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+
10 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao pakuti ndalola iye pamodzi ndi atumiki ake kuumitsa mitima yawo,+ kuti ndichite zizindikiro zanga pamaso pake.+
6 Komanso, mukuumitsiranji mitima yanu mmene Aiguputo ndi Farao anaumitsira mitima yawo?+ Si paja Mulungu atangowakhaulitsa+ analola Aisiraeli kupita, ndipo iwo anapitadi?+