Ekisodo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita kanthawi, panafika mwana wamkazi wa Farao kudzasamba mumtsinje wa Nailo. Ndipo atsikana omutumikira anali kuyenda m’mphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabokosi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+ Ekisodo 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ulawirire m’mawa kwambiri kukakumana ndi Farao.+ Iyetu adzapita kumtsinje, ndipo ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+
5 Patapita kanthawi, panafika mwana wamkazi wa Farao kudzasamba mumtsinje wa Nailo. Ndipo atsikana omutumikira anali kuyenda m’mphepete mwa mtsinjewo. Kenako iye anaona kabokosi kaja kali pakati pa mabango. Nthawi yomweyo anatuma kapolo wake wamkazi kuti akakatenge.+
20 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ulawirire m’mawa kwambiri kukakumana ndi Farao.+ Iyetu adzapita kumtsinje, ndipo ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+