Ekisodo 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+ Yoswa 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko. Salimo 78:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mulungu anawatumizira tizilombo toyamwa magazi kuti tiwadye,+Ndi achule kuti awawononge.+
12 Ine ndidzadutsa m’dziko la Iguputo usiku umenewo+ ndi kupha mwana aliyense woyamba kubadwa m’dziko la Iguputo, mwana wa munthu kapena wa chiweto.+ Ndipo ndidzapereka ziweruzo pa milungu yonse ya mu Iguputo.+ Ine ndine Yehova.+
5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko.