-
Ekisodo 12:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Pamenepo Aisiraeli ananyamula ufa wokanda wa mkate wopanda chofufumitsa. Anaunyamulira m’zokandiramo ufa pamapewa awo atazikulunga m’nsalu zawo.
-