Salimo 78:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Mulungu anawatumizira tizilombo toyamwa magazi kuti tiwadye,+Ndi achule kuti awawononge.+ Salimo 105:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Analamula kuti pagwe tizilombo touluka toyamwa magazi,+Komanso ntchentche zoluma m’madera awo onse.+
31 Analamula kuti pagwe tizilombo touluka toyamwa magazi,+Komanso ntchentche zoluma m’madera awo onse.+