Ekisodo 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 M’chonderereni Yehova kuti aletse mabingu ndi matalala ake.+ Pamenepo ndikulolani kupita, ndipo simukhalanso kuno.”
28 M’chonderereni Yehova kuti aletse mabingu ndi matalala ake.+ Pamenepo ndikulolani kupita, ndipo simukhalanso kuno.”