Ekisodo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Farao anaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Chondererani Yehova+ kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga, pakuti ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”+ Ekisodo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero ndikhululukireni+ tchimo langa kamodzi kokha kano, ndipo chondererani+ Yehova Mulungu wanu kuti andichotsere mliri wakuphawu.” Machitidwe 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha Simoni uja anati: “Amuna inu, ndipemphereni chonde kwa Yehova mopembedzera+ kuti zonse mwanenazo zisandigwere.”
8 Patapita nthawi, Farao anaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Chondererani Yehova+ kuti achotse achule pa ine ndi anthu anga, pakuti ndikufuna kulola anthu anu kuti apite kukapereka nsembe kwa Yehova.”+
17 Chotero ndikhululukireni+ tchimo langa kamodzi kokha kano, ndipo chondererani+ Yehova Mulungu wanu kuti andichotsere mliri wakuphawu.”
24 Poyankha Simoni uja anati: “Amuna inu, ndipemphereni chonde kwa Yehova mopembedzera+ kuti zonse mwanenazo zisandigwere.”