Ekisodo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo ndikukuuza kuti: Lola mwana wanga apite kuti akanditumikire. Koma ngati ukukana kumulola kuti apite, taona ndidzapha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba kubadwa.”’”+ Ekisodo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati upitiriza kukana kuti apite, ndigwetsera dziko lako lonse mliri wa achule.+ Salimo 68:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndithudi, Mulungu adzaphwanya mitu ya adani ake kukhala zibenthuzibenthu,+Adzaphwanya liwombo latsitsi la aliyense woyenda m’njira yochimwa.+ Miyambo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake tsoka lake lidzabwere mwadzidzidzi.+ Adzathyoledwa modzidzimutsa, ndipo sadzachira.+
23 Ndipo ndikukuuza kuti: Lola mwana wanga apite kuti akanditumikire. Koma ngati ukukana kumulola kuti apite, taona ndidzapha mwana wako wamwamuna, mwana wako woyamba kubadwa.”’”+
21 Ndithudi, Mulungu adzaphwanya mitu ya adani ake kukhala zibenthuzibenthu,+Adzaphwanya liwombo latsitsi la aliyense woyenda m’njira yochimwa.+
15 N’chifukwa chake tsoka lake lidzabwere mwadzidzidzi.+ Adzathyoledwa modzidzimutsa, ndipo sadzachira.+