Salimo 78:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anapha mitengo yawo ya mpesa ndi mvula yamatalala.+Anapha mitengo yawo ya mkuyu ndi matalala.+ Salimo 105:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anawagwetsera matalala m’malo mwa mvula,+Anawagwetseranso moto woyaka, walawilawi m’dziko lawo.+