Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 10:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Dzombelo lidzakuta nthaka yonse ndipo simudzatha kuona dothi. Lidzadya chilichonse chotsalira. Ndithu, lidzadya chilichonse chimene matalala anakusiyirani. Ndipo lidzadya mitengo yanu yonse imene yaphuka.+

  • Yobu 38:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi unalowapo munkhokwe ya chipale chofewa,+

      Kapena umaziona nkhokwe za matalala,+

  • Salimo 78:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Anapha mitengo yawo ya mpesa ndi mvula yamatalala.+

      Anapha mitengo yawo ya mkuyu ndi matalala.+

  • Salimo 105:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Anawagwetsera matalala m’malo mwa mvula,+

      Anawagwetseranso moto woyaka, walawilawi m’dziko lawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena