Miyambo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+ Yesaya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+ Luka 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”
6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+
10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+
31 Koma iye anamuuza kuti, ‘Ngati sakumvera Zolemba za Mose+ ndi Zolemba za aneneri, sangathekebe ngakhale wina atauka kwa akufa.’”