Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu a kuno saopa Mulungu,+ andipha ndithu chifukwa cha mkazi wangayu.’+

  • Nehemiya 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno ndinati: “Zimene mukuchitazi si zabwino ayi.+ Kodi simuyenera kuyenda moopa+ Mulungu+ kuti tipewe chitonzo+ cha adani athu, anthu a mitundu ina?+

  • Miyambo 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+

  • Miyambo 14:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Munthu woopa Yehova amakhulupirira Mulungu pa chilichonse,+ ndipo ana a munthu ameneyu adzapeza malo othawirako.+

  • 2 Akorinto 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero okondedwanu, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse+ ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi kapena mzimu,+ kwinaku tikukwaniritsa kukhala oyera poopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena