Rute 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umu ndi mmene Naomi anabwererera kwawo. Anabwerera ndi Rute mkazi wachimowabu, mpongozi wake, kuchokera kudziko la Mowabu.+ Iwo anafika ku Betelehemu+ kumayambiriro kwa nyengo yokolola balere.+
22 Umu ndi mmene Naomi anabwererera kwawo. Anabwerera ndi Rute mkazi wachimowabu, mpongozi wake, kuchokera kudziko la Mowabu.+ Iwo anafika ku Betelehemu+ kumayambiriro kwa nyengo yokolola balere.+