Rute 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+
23 Choncho Rute anapitiriza kukhala pafupi ndi atsikana antchito a Boazi, mpaka pamene anamaliza kukolola balere+ ndi tirigu. Ndipo anapitiriza kukhala ndi apongozi ake.+