Deuteronomo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi. Salimo 148:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu anyamata+ ndi inunso anamwali,+Inu okalamba+ pamodzi ndi ana.+
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi.