Genesis 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo. Genesis 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onse a m’nyumba ya Yosefe, abale ake, ndi a m’nyumba ya bambo ake,+ anapita naye limodzi. Ku Goseni kunangotsala ana awo aang’ono, nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zawo. Ekisodo 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komanso ziweto zathu tipita nazo.+ Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tiyenera kukatengapo zina ndi kukazigwiritsa ntchito polambira Yehova Mulungu wathu.+ Pakali pano sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”+
6 Anatenganso ziweto zawo zonse ndi katundu wawo yense amene anapeza m’dziko la Kanani.+ Potsirizira pake, Yakobo ndi ana ake onse anafika ku Iguputo.
8 Onse a m’nyumba ya Yosefe, abale ake, ndi a m’nyumba ya bambo ake,+ anapita naye limodzi. Ku Goseni kunangotsala ana awo aang’ono, nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zawo.
26 Komanso ziweto zathu tipita nazo.+ Sitidzasiya chiweto ngakhale chimodzi, chifukwa tiyenera kukatengapo zina ndi kukazigwiritsa ntchito polambira Yehova Mulungu wathu.+ Pakali pano sitikudziwa kuti tikapereka chiyani polambira Yehova mpaka titakafika kumeneko.”+