2 Samueli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko. Esitere 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Izi zinali choncho chifukwa Moredekai anali ndi udindo waukulu+ m’nyumba ya mfumu ndipo anatchuka+ m’zigawo zonse chifukwa mphamvu zake zinali kukulirakulira.+ Machitidwe 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.
9 Ine ndidzakhala ndi iwe kulikonse kumene udzapite,+ ndipo ndidzawononga ndi kuchotsa adani ako onse pamaso pako.+ Ndidzakupangira dzina lotchuka,+ lofanana ndi dzina la anthu otchuka amene ali m’dziko.
4 Izi zinali choncho chifukwa Moredekai anali ndi udindo waukulu+ m’nyumba ya mfumu ndipo anatchuka+ m’zigawo zonse chifukwa mphamvu zake zinali kukulirakulira.+
22 Chotero Mose anaphunzira nzeru+ zonse za Aiguputo. Ndipo anali wamphamvu m’mawu+ ndi m’zochita zake.