Numeri 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+ Ezekieli 45:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita pasika.+ Muzichita chikondwerero chimenechi kwa masiku 7 ndipo muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+
21 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo, muzichita pasika.+ Muzichita chikondwerero chimenechi kwa masiku 7 ndipo muzidya mikate yopanda chofufumitsa.+