Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Salimo 105:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anakumbukira lonjezo lake loyera limene analonjeza mtumiki wake Abulahamu.+
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+