Levitiko 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Munthu asapatule nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yoyera, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ng’ombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+
26 “‘Munthu asapatule nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yoyera, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ng’ombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+