Salimo 78:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+ Salimo 135:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+
51 Pamapeto pake anapha ana onse oyamba kubadwa mu Iguputo,+Amene ndi chiyambi cha mphamvu zawo zobereka m’mahema a Hamu.+
8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+