Numeri 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+ Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi. 1 Mbiri 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa, ndipo akukhala kumeneko mpaka lero.
20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+
19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.