Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+
14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+