Ekisodo 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+ Numeri 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo, Mose anapereka dandaulo lawolo pamaso pa Yehova.+
19 Ndipo anthuwo anauza Mose kuti: “Iweyo uzilankhula ndi ife, ndipo ife tizimvetsera, koma Mulungu asalankhule ndi ife kuopera kuti tingafe.”+
8 Ndimalankhula naye pamasom’pamaso,+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa,+ ndipo amaona maonekedwe a Yehova.+ Tsopano n’chifukwa chiyani inu simunaope kum’nena Mose mtumiki wanga?”+