Numeri 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+ Deuteronomo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mukawoloka,+ mulembe pamiyalapo mawu onse a chilamulochi+ kuti mulowe m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, dziko loyenda mkaka ndi uchi, malinga ndi zimene Yehova Mulungu wa makolo anu wakuuzani.+
27 Anauza Mose kuti: “Tinakalowa m’dziko limene munatitumako. Ndithudi ndi dziko loyenda mkaka ndi uchi,+ ndipo zipatso zake ndi izi.+
3 Ndiyeno mukawoloka,+ mulembe pamiyalapo mawu onse a chilamulochi+ kuti mulowe m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, dziko loyenda mkaka ndi uchi, malinga ndi zimene Yehova Mulungu wa makolo anu wakuuzani.+